Eksodo 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anatuma, taonani, sicidafa cingakhale cimodzi comwe ca zoweta za Aisrayeli. Koma mtima wa Farao unauma, ndipo sanalola anthu amuke.

Eksodo 9

Eksodo 9:6-9