Eksodo 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace Yehova anacita cinthuco, ndipo zinafa zoweta zonse za m'Aigupto; koma sicinafa cimodzi conse ca zoweta za ana a Israyeli.

Eksodo 9

Eksodo 9:1-9