Deuteronomo 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akapitao anene ndi anthu, ndi kuti, Ndani munthuyo anamanga nyumba yatsopano, osalowamo? amuke nabwerere kunyumba kwace, kuti angafe kunkhondo nangalowemo munthu wina.

Deuteronomo 20

Deuteronomo 20:1-15