Deuteronomo 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndani munthuyo ananka munda wamphesa osalawa zipatso zace? amuke nabwerere ku nyumba yace, kuti angafe kunkhondo, nangalawe munthu wina zipatso zace.

Deuteronomo 20

Deuteronomo 20:1-15