Deuteronomo 20:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti Yehova Mulungu wanu ndiye wakumuka nanu, kugwirira inu pa adani anu, kukupulumutsani.

Deuteronomo 20

Deuteronomo 20:2-7