2 Mbiri 32:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Hezekiya anadzicepetsa m'kudzikuza kwa mtima wace, iye ndi okhala m'Yerusalemu, momwemo mkwiyo wa Yehova sunawadzera masiku a Hezekiya.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:25-30