2 Mbiri 32:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cuma ndi ulemu zinacurukira Hezekiya, nadzimangira iye zosungiramo siliva, ndi golidi, ndi timiyala ta mtengo wace, ndi zonunkhira, ndi zikopa, ndi zipangizo zokoma ziri zonse;

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:19-32