2 Mbiri 32:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Hezekiya sanabwezera monga mwa cokoma anamcitira, pakuti mtima wace unakwezeka; cifukwa cace unamdzera mkwiyo iye, ndi Yuda, ndi Yerusalemu.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:17-27