2 Mbiri 32:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku omwe aja Hezekiya anadwala pafupi imfa; ndipo anapemphera kwa Yehova; ndi Iye ananena naye, nampatsa cizindikilo codabwiza.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:18-25