2 Mbiri 32:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ambiri anabwera nayo mitulo kwa Yehova ku Yerusalemu, ndi za mtengo wace, kwa Hezekiya mfumu ya Yuda; nakwezeka iye pamaso pa amitundu onse kuyambira pomwepo.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:21-29