2 Mbiri 32:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Yehova analanditsa Hezekiya ndi okhala m'Yerusalemu m'dzanja la Sanakeribu mfumu ya Asuri, ndi m'dzanja la onse ena, nawatsogolera monsemo.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:15-23