Yeremiya 38:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akuru onse anadza kwa Yeremiya, namfunsa; ndipo iye ananena nao monga mwa mau onsewo anamuuza mfumu. Ndipo analeka kunena naye; pakuti sikunamveka mlandu.

Yeremiya 38

Yeremiya 38:26-28