Yeremiya 22:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakuturutsa iwe, ndi mai wako wakubala iwe, kulowa m'dziko lina, limene sunabadwiramo; m'menemo udzafa.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:16-30