Yeremiya 22:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzakupereka iwe m'dzanja la iwo amene afuna moyo wako, m'dzanja la iwo: amene uwaopa, m'dzanja la Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo, m'dzanja la Akasidi.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:18-30