Luka 8:54-56 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

54. Ndipo iye anamgwira dzanja lace, naitana, nati, Buthu, tauka.

55. Ndipo mzimu wace unabwera, ndipo anauka pomwepo; ndipo iye anawauza kuti ampatse kanthu ka kudya.

56. Ndipo atate wace ndi amace anadabwa; ndipo analamulira iwo asauze munthu ali yense cimene cinacitika.

Luka 8