Luka 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anaitana pamodzi khumi ndi awiriwo nawapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse, ndi zakuciritsa nthenda.

Luka 9

Luka 9:1-11