Genesis 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo madzi analinkucepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri.

Genesis 8

Genesis 8:2-12