Ezekieli 40:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'litali mwace mwa khonde mikono makumi awiri, ndi kupingasa kwace mikono khumi ndi umodzi; ndipo panali makwerero khumi okwerera kumeneko; ndipo panali zoimiritsa pa nsanamirazo, imodzi cakuno, ndi imodzi cauko.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:48-49