Eksodo 34:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atatero, ana onse a Israyeli anayandikiza; ndipo iye anawauza zonse Yehova adalankhula naye m'phiri la Sinai.

Eksodo 34

Eksodo 34:29-35