Eksodo 34:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mose anawaitana; ndipo Aroni ndi akazembe onse a khamu la anthu anabwera kwa iye; ndipo Mose analankhula nao.

Eksodo 34

Eksodo 34:26-35