Eksodo 34:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uzibwera nazo zipatso zoyambayamba za nthaka yako ku nyumba ya Yehova Mulungu wako. Usaphika mwana wa mbuzi mu mkaka wa mace.

Eksodo 34

Eksodo 34:24-32