Eksodo 34:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzaingitsa mitundu ya anthu pamaso pako, ndi kukulitsa malire ako; ndipo palibe munthu adzakhumba dziko lako, pakukwera iwe kudzaoneka pamaso pa Yehova Mulungu wako katatu caka cimodzi.

Eksodo 34

Eksodo 34:23-28