Ahebri 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti cihema cidakonzeka, coyamba cija, m'menemo munali coikapo nyali, ndi gome, ndi mkate woonekera; paja paitanidwa Malo Opatulika,

Ahebri 9

Ahebri 9:1-3