2 Mbiri 32:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nasonkhana anthu ambiri, natseka akasupe onse, ndi mtsinje woyenda pakati pa dziko, ndi kuti, Angafike mafumu a Asuri ndi kupeza madzi ambiri.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:1-5