2 Mbiri 32:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanenera Mulungu wa Yerusalemu, monga umo amanenera milungu ya mitundu ya anthu a pa dziko lapansi, ndiyo nchito ya manja a anthu.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:14-22