2 Mbiri 32:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapfuula ndi mau akuru m'cinenedwe ca Ayuda kwa anthu a m'Yerusalemu okhala palinga, kuwaopsa ndi kuwabvuta, kuti alande mudziwu.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:11-21