2 Mbiri 32:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi uti mwa milungu yonse ya mitunduyi ya anthu, amene makolo anga anawaononga konse, unakhoza kulanditsa anthu ace m'dzanja mwanga, kuti Mulungu wako adzakhoza kukulanditsa iwe m'dzanja mwanga?

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:6-15