2 Mbiri 32:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Simudziwa kodi comwe ine ndi makolo anga tacitira anthu onse a m'maikomo? Kodi milungu ya mitundu ya anthu inakhoza konse kulanditsa dziko lao m'dzanja langa?

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:10-14