1 Mafumu 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Solomo anakonda akazi ambiri acilendo, pamodzi ndi mwana wamkazi wa Farao, akazi a ku Moabu, ndi a ku Amoni, ndi a ku Edomu, ndi a ku Zidoni, ndi Ahiti;

1 Mafumu 11

1 Mafumu 11:1-10