Zekariya 12:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Katundu wa mau a Yehova wakunena Israyeli.Atero Yehova, wakuyala miyamba, ndi kuika maziko a dziko lapansi, ndi kulenga mzimu wa munthu m'kati mwace;

2. Taonani, ndidzaika Yerusalemu akhale cipanda codzandiritsa kwa mitundu yonse ya anthu yozungulirapo, ndipo cidzafikira Yuda yemwe pomangira misasa Yerusalemu.

Zekariya 12