Zefaniya 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzacitika tsiku la nsembe ya Yehova, kuti ndidzalanga akalonga ndi ana a mfumu, ndi onse akubvala cobvala cacilendo.

Zefaniya 1

Zefaniya 1:1-16