Yoswa 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anang'amba zobvala zace, nagwa nkhope yace pansi, ku likasa la Yehova, mpaka madzulo, iye ndi akulu akulu a Israyeli, nathira pfumbi pamitu pao.

Yoswa 7

Yoswa 7:1-10