Yoswa 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Lero Uno ndakukunkhunizirani mtonzo wa Aigupto, Cifukwa cace dzina la malowo analicha Giligala kufikira lero lino.

Yoswa 5

Yoswa 5:8-15