Yoswa 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cifukwa cakuti Yoswa anawadula ndi ici: anthu onse oturuka m'Aigupto, anthu amuna, ndiwo amuna onse ankhondo, adafa m'cipululu panjira, ataturuka m'Aigupto.

Yoswa 5

Yoswa 5:1-11