Yoswa 24:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa ananena ndi anthu, Inu mwadzicitira mboni inu nokha kuti mwadzisankhira Yehova kumtumikira iye. Ndipo anati, Ndife mboni.

Yoswa 24

Yoswa 24:21-29