Yoswa 22:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati,

2. nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mosemtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu;

3. simunasiya abale anu masiku awa ambiri mpaka lero lino, koma mwasunga cisungire lamulola Yehova Mulungu wanu.

Yoswa 22