Yoswa 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akamlondola wolipsa mwazi, asampereke m'dzanja lace wakupha mnzaceyo; pakuti anakantha mnansi wace mosadziwa, osamuda kale.

Yoswa 20

Yoswa 20:2-9