Yoswa 19:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kucokera ku Saridi anazungulira kumka kum'mawa kumaturukira dzuwa, mpaka malire a Kisilotu-tabori; naturuka kumka ku Daberati, nakwera ku Yafia;

Yoswa 19

Yoswa 19:9-13