Yoswa 15:57-59 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

57. Kaini, Gibea ndi Timina; midzi khumi pamodzi ndi miraga yao.

58. Haluli, Beti-zuru, ndi Gedori,

59. ndi Maaratu, ndi Bete-anotu, ndi Elitekoni; midzi isanu ndi umodzi pamodzi ndi miraga yao.

Yoswa 15