Yoswa 15:46-50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

46. kuyambira ku Ekroni mpaka kunyanja, yonse ya ku mbali ya Asidodo, pamodzi ndi miraga yao.

47. Asidodo, midzi yace ndi miraga yace; Gaza, midzi yace ndi miraga yace; mpaka mtsinje wa Aigupto, ndi nyanja yaikuru ndi malire ace.

48. Ndi kumapiri Samiri, ndi Yatiri, om Soko;

49. ndi Dana, ndi Kiriyatisana, ndiwo Dibiri;

50. ndi Anabi, ndi Esitemo, ndi Animu;

Yoswa 15