Yoswa 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma abale anga amene anakwera nane anasungunutsa mitima ya anthu; koma ine ndinamtsata Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.

Yoswa 14

Yoswa 14:6-15