Yoswa 13:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire ao anayambira ku Mahanaimu, Basana lonse, ufumu wonse wa Ogi mfumu ya ku Basana, ndi midzi yonse ya Yairi, yokhala m'Basana, midzi makumi asanu ndi limodzi;

Yoswa 13

Yoswa 13:20-32