Yona 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mau awa anafikira mfumu ya Nineve, ndipo Inanyamuka ku mpando wace wacifumu, nibvula copfunda cace, nipfunda ciguduli, nikhala m'mapulusa.

Yona 3

Yona 3:3-7