Yohane 9:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anati kwa iwo, Mukadakhala osaona simukadakhala nalo cimo; koma tsopano munena, kuti, Tipenya: cimo lanu likhala.

Yohane 9

Yohane 9:32-41