Yohane 8:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ayuda anati kwa Iye, Tsopano tazindikira kuti muli ndi ciwanda. 10 Abrahamu anamwalira, ndi aneneri; ndipo Inu munena, Munthu akasunga mau anga, sadzalawa imfa ku nthawi yonse.

Yohane 8

Yohane 8:47-57