Yohane 8:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano mufuna kundipha Ine, ndine munthu amene ndinalankhula ndi inu coonadi, 3 cimene ndinamva kwa Mulungu; ici Abrahamu sanacita.

Yohane 8

Yohane 8:33-41