Yohane 8:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yesu anati, Pamene mutadzamkweza Mwana wa munthu, pomwepo mudzazindikira kuti Ine ndine, ndipo sindicita kanthu kwa Ine ndekha, koma monga anandiphunzitsa Atate, ndilankhula izi.

Yohane 8

Yohane 8:23-32