Yohane 8:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiri nazo zambiri zakulankhula ndi zakuweruza za inu; koma wondituma Ine ali woona; ndipo zimene ndazimva kwa iye, zomwezo ndilankhuia kwa dziko lapansi.

Yohane 8

Yohane 8:19-33