Yohane 8:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anatinso kwa iwo; Ndimuka Ine, ndipo mudzandifuna, ndipo m'cimo lanu mudzafa: kumene ndimukako Ine, simudziwa kudza inu.

Yohane 8

Yohane 8:17-27