Yohane 8:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ananena ndi iye, Ali kuti Atate, wanu? Yesu anayankha, Simudziwa kapena Ine, kapena Atate wanga; mukadadziwa Ine, mukada-dziwanso Atate wanga.

Yohane 8

Yohane 8:16-25